-
2 Timoteyo 3:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ena mwa anthuwa amalowerera mozemba mʼmabanja nʼkumachititsa amayi ena kuti akhale akapolo awo. Amayiwa amakhala ofooka chifukwa cha machimo awo ndiponso otengeka ndi zilakolako zosiyanasiyana.
-