2 Timoteyo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Ambuye anaima nane pafupi nʼkundipatsa mphamvu. Anachita zimenezi kuti kudzera mwa ine, ntchito yolalikira ichitike mokwanira, ndi kuti mitundu yonse ya anthu imve uthengawo.+ Ndiponso ndinapulumutsidwa mʼkamwa mwa mkango.+ 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:17 Nsanja ya Olonda,4/15/2015, ptsa. 24-26, 28
17 Koma Ambuye anaima nane pafupi nʼkundipatsa mphamvu. Anachita zimenezi kuti kudzera mwa ine, ntchito yolalikira ichitike mokwanira, ndi kuti mitundu yonse ya anthu imve uthengawo.+ Ndiponso ndinapulumutsidwa mʼkamwa mwa mkango.+