Tito 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma pa nthawi yake, anachititsa kuti mawu ake adziwike kudzera mu ntchito yolalikira imene ndinapatsidwa+ mogwirizana ndi lamulo la Mpulumutsi wathu, Mulungu.
3 Koma pa nthawi yake, anachititsa kuti mawu ake adziwike kudzera mu ntchito yolalikira imene ndinapatsidwa+ mogwirizana ndi lamulo la Mpulumutsi wathu, Mulungu.