-
Tito 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndinakusiya ku Kerete kuti ukonze zinthu zolakwika komanso uike akulu mumzinda uliwonse, mogwirizana ndi malangizo amene ndinakupatsa.
-