Tito 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Popeza ndi mtumiki* wa Mulungu, woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera. Asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa, wankhanza* kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo. Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Gulu, ptsa. 32-33, 35-36 Nsanja ya Olonda,12/15/2012, tsa. 1010/15/1996, tsa. 157/1/1996, tsa. 79/1/1990, ptsa. 24, 25-26, 27-28 Galamukani!,5/8/1992, ptsa. 22-23
7 Popeza ndi mtumiki* wa Mulungu, woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera. Asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa, wankhanza* kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.
1:7 Gulu, ptsa. 32-33, 35-36 Nsanja ya Olonda,12/15/2012, tsa. 1010/15/1996, tsa. 157/1/1996, tsa. 79/1/1990, ptsa. 24, 25-26, 27-28 Galamukani!,5/8/1992, ptsa. 22-23