Tito 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zosathandiza ndiponso opusitsa ena, ndipo pakati pa anthu amenewa palinso amene akulimbikitsabe mdulidwe.+ Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,10/15/2007, ptsa. 25-26
10 Chifukwa pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zosathandiza ndiponso opusitsa ena, ndipo pakati pa anthu amenewa palinso amene akulimbikitsabe mdulidwe.+