Tito 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zinthu zonse nʼzoyera kwa anthu oyera.+ Koma kwa anthu oipitsidwa ndi opanda chikhulupiriro kulibe choyera, chifukwa maganizo awo ndi chikumbumtima chawo nʼzoipitsidwa.+ Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, tsa. 3010/15/2007, ptsa. 25-27
15 Zinthu zonse nʼzoyera kwa anthu oyera.+ Koma kwa anthu oipitsidwa ndi opanda chikhulupiriro kulibe choyera, chifukwa maganizo awo ndi chikumbumtima chawo nʼzoipitsidwa.+