-
Tito 2:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Amuna achikulire akhale osachita zinthu mopitirira malire, opanda chibwana, oganiza bwino, achikhulupiriro cholimba, achikondi chachikulu ndi opirira kwambiri.
-