Tito 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukhale chitsanzo pa ntchito zabwino mʼnjira iliyonse. Uziphunzitsa zolondola* ndipo uzisonyeza kuti ndiwe wopanda chibwana.+ Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Nsanja ya Olonda,6/15/1994, tsa. 21
7 Ukhale chitsanzo pa ntchito zabwino mʼnjira iliyonse. Uziphunzitsa zolondola* ndipo uzisonyeza kuti ndiwe wopanda chibwana.+