Tito 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu waonetsa kukoma mtima kwake kwakukulu kumene kumabweretsa chipulumutso kwa anthu, kaya akhale otani.+ Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,11/1/1997, ptsa. 11-13 Kukambitsirana, tsa. 95
11 Mulungu waonetsa kukoma mtima kwake kwakukulu kumene kumabweretsa chipulumutso kwa anthu, kaya akhale otani.+