-
Tito 3:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Paja nafenso poyamba tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako zosiyanasiyana ndiponso a zinthu zosangalatsa, ochita zoipa, akaduka, onyansa komanso tinkadana.
-