Tito 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iwe uzipewa kutsutsana pa zinthu zopusa komanso zokhudza mibadwo ya makolo. Uzipewanso kukangana ndi kulimbana ndi anthu pa nkhani zokhudza Chilamulo, chifukwa zimenezi nʼzosathandiza ndiponso zopanda phindu.+
9 Koma iwe uzipewa kutsutsana pa zinthu zopusa komanso zokhudza mibadwo ya makolo. Uzipewanso kukangana ndi kulimbana ndi anthu pa nkhani zokhudza Chilamulo, chifukwa zimenezi nʼzosathandiza ndiponso zopanda phindu.+