-
Tito 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Onse amene ndili nawo kuno akupereka moni. Undiperekere moni kwa anthu amene amatikonda chifukwa tili ndi chikhulupiriro chofanana.
Kukoma mtima kwakukulu kukhale ndi nonsenu.
-