Filimoni 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sukhala nayenso monga kapolo,+ koma akhalanso mʼbale wokondedwa,+ amene ine ndimamukonda kwambiri. Koma iweyo uyenera kumukonda koposa pamenepo chifukwa ndi kapolo wako komanso mʼbale wako mwa Ambuye. Filimoni Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, tsa. 312/15/1991, tsa. 23
16 Sukhala nayenso monga kapolo,+ koma akhalanso mʼbale wokondedwa,+ amene ine ndimamukonda kwambiri. Koma iweyo uyenera kumukonda koposa pamenepo chifukwa ndi kapolo wako komanso mʼbale wako mwa Ambuye.