-
Filimoni 19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ine Paulo, ndikulemba ndi dzanja langa: Ndidzabweza ngongoleyo. Ndipo sindikufunikira kuchita kukuuza zimenezi, paja iwenso uli ndi ngongole kwa ine ya moyo wako.
-