Aheberi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kalekale, Mulungu ankalankhula ndi makolo athu kudzera mwa aneneri. Anachita zimenezi kambirimbiri ndiponso mʼnjira zosiyanasiyana.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54
1 Kalekale, Mulungu ankalankhula ndi makolo athu kudzera mwa aneneri. Anachita zimenezi kambirimbiri ndiponso mʼnjira zosiyanasiyana.+