Aheberi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako”?+ Komanso kuti: “Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+
5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako”?+ Komanso kuti: “Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+