Aheberi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndi mpando wako wachifumu+ mpaka kalekale ndipo ndodo ya Ufumu wako, ndi ndodo yachilungamo. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 6 Kukambitsirana, ptsa. 408-409
8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndi mpando wako wachifumu+ mpaka kalekale ndipo ndodo ya Ufumu wako, ndi ndodo yachilungamo.