Aheberi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsochi pogwiritsa ntchito zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mzimu woyera umene anaupereka mogwirizana ndi chifuniro chake.+
4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsochi pogwiritsa ntchito zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mzimu woyera umene anaupereka mogwirizana ndi chifuniro chake.+