Aheberi 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima kwambiri, ngati mmene zinalili pa tsiku limene anandiyesa mʼchipululu.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:8 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, ptsa. 12-13
8 musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima kwambiri, ngati mmene zinalili pa tsiku limene anandiyesa mʼchipululu.+