Aheberi 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mʼmalomwake, pitirizani kulimbikitsana tsiku ndi tsiku, nthawi iliyonse imene mukuti “Lero,”+ kuti chinyengo champhamvu cha uchimo chisaumitse mtima wa aliyense wa inu. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,1/1/1998, tsa. 8
13 Mʼmalomwake, pitirizani kulimbikitsana tsiku ndi tsiku, nthawi iliyonse imene mukuti “Lero,”+ kuti chinyengo champhamvu cha uchimo chisaumitse mtima wa aliyense wa inu.