Aheberi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma nʼkupsetsa mtima Mulungu? Kodi si anthu onse amene anatuluka mʼdziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+
16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma nʼkupsetsa mtima Mulungu? Kodi si anthu onse amene anatuluka mʼdziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+