Aheberi 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, popeza tili ndi mkulu wa ansembe wapamwamba, Yesu Mwana wa Mulungu,+ amene anapita kumwamba, tiyeni tipitirize kulengeza zoti timamukhulupirira.+
14 Choncho, popeza tili ndi mkulu wa ansembe wapamwamba, Yesu Mwana wa Mulungu,+ amene anapita kumwamba, tiyeni tipitirize kulengeza zoti timamukhulupirira.+