Aheberi 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pofika pano munayenera kukhala aphunzitsi. Koma sizili choncho, ndipo mukufunikanso wina woti akuphunzitseni mfundo zoyambirira+ za mʼmawu opatulika a Mulungu, kuyambira pachiyambi. Inu mwayambanso kufuna mkaka, osati chakudya chotafuna. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, tsa. 25 Kuphunzitsa, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, ptsa. 16-175/15/2010, tsa. 221/1/1998, ptsa. 8-94/15/1997, ptsa. 28-291/1/1996, tsa. 298/15/1993, ptsa. 14-168/1/1992, tsa. 9
12 Pofika pano munayenera kukhala aphunzitsi. Koma sizili choncho, ndipo mukufunikanso wina woti akuphunzitseni mfundo zoyambirira+ za mʼmawu opatulika a Mulungu, kuyambira pachiyambi. Inu mwayambanso kufuna mkaka, osati chakudya chotafuna.
5:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, tsa. 25 Kuphunzitsa, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, ptsa. 16-175/15/2010, tsa. 221/1/1998, ptsa. 8-94/15/1997, ptsa. 28-291/1/1996, tsa. 298/15/1993, ptsa. 14-168/1/1992, tsa. 9