Aheberi 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa Levi anali asanabadwe pamene kholo lake Abulahamu anakumana ndi Melekizedeki, koma anali woti adzakhala mbadwa ya Abulahamuyo.+
10 Chifukwa Levi anali asanabadwe pamene kholo lake Abulahamu anakumana ndi Melekizedeki, koma anali woti adzakhala mbadwa ya Abulahamuyo.+