Aheberi 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ponena kuti “pangano latsopano,” iye wachititsa kuti loyambalo lithe ntchito.+ Pangano limene latha ntchito ndipo likukalamba, ndiye kuti latsala pangʼono kufafanizika.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Nsanja ya Olonda,10/15/2014, ptsa. 15-16 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 100-103
13 Ponena kuti “pangano latsopano,” iye wachititsa kuti loyambalo lithe ntchito.+ Pangano limene latha ntchito ndipo likukalamba, ndiye kuti latsala pangʼono kufafanizika.+