Aheberi 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Khristu sanalowe mʼmalo oyera opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Panopa iye ali kumwamba kuti azionekera pamaso pa Mulungu mʼmalo mwa ifeyo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:24 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 183-184 Nsanja ya Olonda,8/1/2011, tsa. 271/15/2000, ptsa. 15-162/15/1991, ptsa. 15-17
24 Khristu sanalowe mʼmalo oyera opangidwa ndi manja a anthu,+ amene ndi chithunzi cha malo enieniwo,+ koma analowa kumwamba kwenikweniko.+ Panopa iye ali kumwamba kuti azionekera pamaso pa Mulungu mʼmalo mwa ifeyo.+
9:24 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 183-184 Nsanja ya Olonda,8/1/2011, tsa. 271/15/2000, ptsa. 15-162/15/1991, ptsa. 15-17