-
Aheberi 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Zikanakhala choncho, kodi nsembezo sakanasiya kuzipereka? Akanasiya chifukwa zikanakhala kuti anthu ochita utumiki wopatulikawo ayeretsedwa, sakanakhalanso ndi chikumbumtima chakuti ndi ochimwa.
-