Aheberi 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tiyeni tifike kwa Mulungu ndi mtima wonse komanso tili ndi chikhulupiriro chonse, chifukwa mitima yathu yayeretsedwa* kuti tisakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa mʼmadzi oyera.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:22 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, ptsa. 19-20
22 tiyeni tifike kwa Mulungu ndi mtima wonse komanso tili ndi chikhulupiriro chonse, chifukwa mitima yathu yayeretsedwa* kuti tisakhalenso ndi chikumbumtima choipa,+ ndipo matupi athu asambitsidwa mʼmadzi oyera.+