Aheberi 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa cha chikhulupiriro, ankakhala monga mlendo mʼdziko limene analonjezedwa.+ Iye ankakhala mʼmatenti+ pamodzi ndi Isaki ndi Yakobo, amenenso Mulungu anawalonjeza kuti adzawapatsa dzikoli.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2020, ptsa. 3-4 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 16-177/1/1989, tsa. 20
9 Chifukwa cha chikhulupiriro, ankakhala monga mlendo mʼdziko limene analonjezedwa.+ Iye ankakhala mʼmatenti+ pamodzi ndi Isaki ndi Yakobo, amenenso Mulungu anawalonjeza kuti adzawapatsa dzikoli.+
11:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2020, ptsa. 3-4 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 16-177/1/1989, tsa. 20