-
Aheberi 11:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Komabe ngakhale kuti onsewa Mulungu anawapatsa umboni wakuti akusangalala nawo chifukwa cha chikhulupiriro chawo, sanaone kukwaniritsidwa kwa lonjezolo.
-