Aheberi 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo mwaiwaliratu malangizo okudandaulirani ngati amene bambo amauza ana ake kuti: “Mwana wanga, usapeputse chilango* cha Yehova,* kapena kutaya mtima pamene iye akukudzudzula. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:5 Nsanja ya Olonda,3/15/2012, tsa. 2912/15/1989, ptsa. 13-14
5 Ndipo mwaiwaliratu malangizo okudandaulirani ngati amene bambo amauza ana ake kuti: “Mwana wanga, usapeputse chilango* cha Yehova,* kapena kutaya mtima pamene iye akukudzudzula.