Aheberi 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muyenera kupirira kuti muphunzitsidwe.* Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samupatsa chilango?+
7 Muyenera kupirira kuti muphunzitsidwe.* Mulungu akuchita nanu zinthu ngati ana ake.+ Ndi mwana wanji amene bambo ake samupatsa chilango?+