Aheberi 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa bambo athu otiberekawo, anatilanga kwa nthawi yochepa mogwirizana ndi zimene ankaziona kuti nʼzoyenera, koma Mulungu amatilanga kuti zinthu zitiyendere bwino ndiponso kuti tikhale oyera ngati iyeyo.+
10 Chifukwa bambo athu otiberekawo, anatilanga kwa nthawi yochepa mogwirizana ndi zimene ankaziona kuti nʼzoyenera, koma Mulungu amatilanga kuti zinthu zitiyendere bwino ndiponso kuti tikhale oyera ngati iyeyo.+