Aheberi 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 komanso limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake+ ndipo anthu atawamva, anapempha kuti asawauzenso mawu ena.+
19 komanso limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake+ ndipo anthu atawamva, anapempha kuti asawauzenso mawu ena.+