23 pamsonkhano wawo waukulu.+ Kumenenso kuli mpingo wa woyamba kubadwayo, mpingo wa iwo amene mayina awo alembedwa kumwamba. Kumeneko kulinso Mulungu, Woweruza wa onse.+ Kulinso olungama amene akukhala ndi moyo mogwirizana ndi mphamvu ya mzimu woyera+ omwe athandizidwa kukhala angwiro.+