Yakobo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo wachuma asangalale chifukwa waphunzira kukhala wodzichepetsa,+ chifukwa mofanana ndi duwa lakutchire, iye adzafota. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 9-10
10 ndipo wachuma asangalale chifukwa waphunzira kukhala wodzichepetsa,+ chifukwa mofanana ndi duwa lakutchire, iye adzafota.