Yakobo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwakufuna kwake, iye anatibereka pamene tinakhulupirira mawu ake omwe ndi choonadi.+ Anachita zimenezi kuti tikhale zipatso zoyambirira pa zolengedwa zake.+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Nsanja ya Olonda,1/1/2007, tsa. 2211/15/1997, tsa. 11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 202-203
18 Mwakufuna kwake, iye anatibereka pamene tinakhulupirira mawu ake omwe ndi choonadi.+ Anachita zimenezi kuti tikhale zipatso zoyambirira pa zolengedwa zake.+