Yakobo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiye mukamachita zimenezi, kodi simukusonyeza tsankho pakati panu?+ Ndipo kodi pamenepa simunakhale oweruza amene akupereka zigamulo zoipa?+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 14
4 Ndiye mukamachita zimenezi, kodi simukusonyeza tsankho pakati panu?+ Ndipo kodi pamenepa simunakhale oweruza amene akupereka zigamulo zoipa?+