Yakobo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani abale anga okondedwa. Kodi Mulungu sanasankhe anthu amene dzikoli limawaona kuti ndi osauka kuti akhale olemera mʼchikhulupiriro+ komanso kuti akhale oyenera kupatsidwa Ufumu umene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda?+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 14
5 Tamverani abale anga okondedwa. Kodi Mulungu sanasankhe anthu amene dzikoli limawaona kuti ndi osauka kuti akhale olemera mʼchikhulupiriro+ komanso kuti akhale oyenera kupatsidwa Ufumu umene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda?+