Yakobo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma inu simukulemekeza anthu osauka. Kodi si olemera amene amakuvutitsani+ komanso kukupititsani kumabwalo amilandu? Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 14
6 Koma inu simukulemekeza anthu osauka. Kodi si olemera amene amakuvutitsani+ komanso kukupititsani kumabwalo amilandu?