Yakobo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa amene ananena kuti, “Musachite chigololo,”+ ananenanso kuti, “Musaphe munthu.”+ Ndiye ngati iwe sunachite chigololo koma wapha munthu, ndiye kuti walakwira chilamulo. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 14
11 Chifukwa amene ananena kuti, “Musachite chigololo,”+ ananenanso kuti, “Musaphe munthu.”+ Ndiye ngati iwe sunachite chigololo koma wapha munthu, ndiye kuti walakwira chilamulo.