Yakobo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzilankhula komanso kuchita zinthu ngati anthu amene adzaweruzidwe ndi chilamulo cha anthu amene ali pa ufulu.*+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 149/1/1996, tsa. 15
12 Muzilankhula komanso kuchita zinthu ngati anthu amene adzaweruzidwe ndi chilamulo cha anthu amene ali pa ufulu.*+