Yakobo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 koma wina mwa inu nʼkumuuza kuti, “Uyende bwino, upeze zovala ndi zakudya za tsiku lililonse,” koma osamupatsa zimene akufunikirazo kuti akhale ndi moyo, kodi pali phindu lanji?+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:16 Nsanja ya Olonda,5/1/2001, tsa. 511/15/1997, ptsa. 14-1510/15/1986, ptsa. 15-29
16 koma wina mwa inu nʼkumuuza kuti, “Uyende bwino, upeze zovala ndi zakudya za tsiku lililonse,” koma osamupatsa zimene akufunikirazo kuti akhale ndi moyo, kodi pali phindu lanji?+