Yakobo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho lemba linakwaniritsidwa limene limati: “Abulahamu anakhulupirira zimene Yehova* anamuuza ndipo ankaonedwa kuti ndi wolungama,”+ choncho ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova.*+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:23 Nsanja ya Olonda,8/15/1998, ptsa. 11-1211/15/1997, tsa. 15 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 73-75
23 Choncho lemba linakwaniritsidwa limene limati: “Abulahamu anakhulupirira zimene Yehova* anamuuza ndipo ankaonedwa kuti ndi wolungama,”+ choncho ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova.*+
2:23 Nsanja ya Olonda,8/15/1998, ptsa. 11-1211/15/1997, tsa. 15 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 73-75