Yakobo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mofanana ndi zimenezi, kodi Rahabi amene anali hule uja, sanaonedwenso kuti ndi wolungama chifukwa cha ntchito zake, atalandira bwino anthu amene ankafufuza dziko lawo nʼkuwathandiza kuti athawe kudzera njira ina?+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2023, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,11/1/2013, tsa. 1411/15/1997, ptsa. 15-1612/15/1993, ptsa. 22-2512/15/1986, tsa. 20
25 Mofanana ndi zimenezi, kodi Rahabi amene anali hule uja, sanaonedwenso kuti ndi wolungama chifukwa cha ntchito zake, atalandira bwino anthu amene ankafufuza dziko lawo nʼkuwathandiza kuti athawe kudzera njira ina?+
2:25 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2023, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,11/1/2013, tsa. 1411/15/1997, ptsa. 15-1612/15/1993, ptsa. 22-2512/15/1986, tsa. 20