-
Yakobo 3:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Anthu angathe kuweta mtundu uliwonse wa nyama zakutchire, mbalame, nyama zokwawa ndiponso zamoyo zamʼnyanja ndipo akhala akuchita zimenezi.
-