Yakobo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Lilime timaligwiritsa ntchito potamanda Yehova,* amene ndi Atate, komanso ndi lilime lomwelo timatemberera anthu amene analengedwa “mʼchifaniziro cha Mulungu.”+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, ptsa. 17-187/15/1993, tsa. 21
9 Lilime timaligwiritsa ntchito potamanda Yehova,* amene ndi Atate, komanso ndi lilime lomwelo timatemberera anthu amene analengedwa “mʼchifaniziro cha Mulungu.”+