Yakobo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngati mʼmitima yanu muli nsanje yaikulu+ ndi kukonda mikangano,*+ musadzitame+ chifukwa kuchita zimenezo nʼkunamizira choonadi. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,3/15/2008, ptsa. 22-2311/15/1997, tsa. 18
14 Koma ngati mʼmitima yanu muli nsanje yaikulu+ ndi kukonda mikangano,*+ musadzitame+ chifukwa kuchita zimenezo nʼkunamizira choonadi.