Yakobo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi nkhondo ndi ndewu zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Kodi sizikuchokera mʼzilakolako za thupi lanu zimene zikulimbana kuti zizilamulira matupi anu?*+ Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,9/1/1998, tsa. 1211/15/1997, tsa. 199/15/1995, tsa. 4
4 Kodi nkhondo ndi ndewu zimene zikuchitika pakati panu zikuchokera kuti? Kodi sizikuchokera mʼzilakolako za thupi lanu zimene zikulimbana kuti zizilamulira matupi anu?*+